Favorite New Song in Chichewa
Palibe wo fana ndi Yesu,
Palibe wo fana nyae,
Palibe wo fana ndi Yesu,
Sadza, peze, kanso! (2x)
Ndayenda yenda konse konse,
Ndazungalira konse, konse,
Ndafuna funa konse, konse,
Sadza, peze, kanso!
Palibe wo fana ndi Yesu,
Palibe wo fana nyae,
Palibe wo fana ndi Yesu,
Sadza, peze, kanso! (2x)
Ndayenda yenda konse konse,
Ndazungalira konse, konse,
Ndafuna funa konse, konse,
Sadza, peze, kanso!